Yohane 1:10-11

Yohane 1:10-11 CCL

Iye anali mʼdziko lapansi, ndipo ngakhale kuti dziko lapansi linalengedwa ndi Iye, dziko lapansilo silinamuzindikire Iye. Iye anabwera kwa iwo amene anali akeake, koma akewo sanamulandire Iye.