YouVersion 로고
성경묵상동영상
앱 다운로드
언어 선택
검색 아이콘

GENESIS 8 - 인기 성경 구절

1

GENESIS 8:21-22

Buku Lopatulika

BLP-2018

Ndipo Yehova anamva chonunkhira chakukondweretsa; nati Yehova m'mtima mwake, Sindidzatembereranso konse nthaka chifukwa cha munthu; pakuti ndingaliro ya mtima wa munthu ili yoipa kuyambira pa unyamata wake; sindidzaphanso konse zinthu zonse zamoyo, monga momwe ndachitiramo. Pakukhalabe masiku a dziko lapansi, nthawi yakubzala ndi yakukunkha, chisanu ndi mafundi, malimwe ndi msakasa, usana ndi usiku sizidzalekai.

비교

GENESIS 8:21-22 살펴보기

2

GENESIS 8:20

Buku Lopatulika

BLP-2018

Ndipo Nowa anamanga guwa la nsembe la Yehova; natengapo nyama zodyedwa zonse ndi mbalame zodyedwa zonse napereka nsembe zopsereza paguwapo.

비교

GENESIS 8:20 살펴보기

3

GENESIS 8:1

Buku Lopatulika

BLP-2018

Ndipo Mulungu anakumbukira Nowa ndi zamoyo zonse, ndi nyama zonse zimene zinali pamodzi naye m'chingalawamo; ndipo Mulungu anapititsa mphepo padziko lapansi, naphwa madzi

비교

GENESIS 8:1 살펴보기

4

GENESIS 8:11

Buku Lopatulika

BLP-2018

ndipo njiwa inadza kwa iye madzulo; ndipo, taonani, m'kamwa mwake munali tsamba la azitona lothyoledwa: ndipo anadziwa Nowa kuti madzi analimkuphwa padziko lapansi.

비교

GENESIS 8:11 살펴보기

GENESIS 8: 관련 무료 묵상 계획

이전 장
다음 장
YouVersion

매일 하나님과 친밀하게 동행하도록 격려하고 도전하기.

사역

소개

채용 정보

자원 봉사

블로그

기사

유용한 링크

도움

후원

성경 번역본

오디오 성경

성경 언어

오늘의 말씀


디지털 사역

Life.Church
English (US)

©2025 Life.Church / YouVersion

개인 정보 취급 정책약관
취약점 공개 프로그램
페이스북트위터인스타그램유튜브핀터레스트

홈

성경

묵상

동영상