1
GENESIS 25:23
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Yehova ndipo anati kwa iye, Mitundu iwiri ili m'mimba mwako, magulu awiri a anthu adzatuluka m'mimba mwako; gulu lina lidzapambana mphamvu ndi linzake; wamkulu adzakhala kapolo wa wamng'ono.
Compare
GENESIS 25:23 ખોજ કરો
2
GENESIS 25:30
ndipo Esau anati kwa Yakobo, Undipatse ndidye chofiiracho; chifukwa ndalefuka: chifukwa chake anamutcha dzina lake Edomu.
GENESIS 25:30 ખોજ કરો
3
GENESIS 25:21
Ndipo Isaki anampembedzera mkazi wake kwa Yehova popeza anali wouma: ndipo Yehova analola kupembedza kwake, ndipo Rebeka mkazi wake anatenga pakati.
GENESIS 25:21 ખોજ કરો
4
GENESIS 25:32-33
Ndipo Esau anati, Taona, ine ndifuna kufa: ukuluwo ndidzapindulanji nao? Ndipo anati Yakobo, Undilumbirire ine lero lomwe, ndipo analumbirira iye; nagulana ndi Yakobo ukulu wake.
GENESIS 25:32-33 ખોજ કરો
5
GENESIS 25:26
Pambuyo pake ndipo anabadwa mphwake ndipo dzanja lake linagwira chitende cha Esau, ndi dzina lake linatchedwa Yakobo: ndipo Isaki anali wa zaka makumi asanu ndi limodzi pamene mkazi wake anabala iwo.
GENESIS 25:26 ખોજ કરો
6
GENESIS 25:28
Ndipo Isaki anakonda Esau, chifukwa anadya nyama yake ya m'thengo; koma Rebeka anakonda Yakobo.
GENESIS 25:28 ખોજ કરો
હોમ
બાઇબલ
યોજનાઓ
વિડિઓઝ