1
GENESIS 15:6
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo anakhulupirira Yehova, ndipo kunayesedwa kwa iye chilungamo.
Compare
GENESIS 15:6 ખોજ કરો
2
GENESIS 15:1
Zitapita izo, mau a Yehova anadza kwa Abramu m'masomphenya, kuti, Usaope, Abramu, Ine ndine chikopa chako ndi mphotho yako yaikulukulu.
GENESIS 15:1 ખોજ કરો
3
GENESIS 15:5
Ndipo anamtulutsa iye kunja, nati, Tayang'anatu kumwamba, uwerenge nyenyezi, ngati ukhoza kuziwerenga zimenezo: ndipo anati kwa iye, Zoterezo zidzakhala mbeu zako.
GENESIS 15:5 ખોજ કરો
4
GENESIS 15:4
Ndipo, taonani, mau a Yehova anadza kwa iye kuti, Uyu sadzakhala wakulowa m'malo mwako; koma iye amene adzatuluka m'chuuno mwako, ndiye adzakhala wakulowa m'malo mwako.
GENESIS 15:4 ખોજ કરો
5
GENESIS 15:13
Ndipo anati kwa Abramu, Dziwitsa ndithu kuti mbeu zako zidzakhala alendo m'dziko la eni, nizidzatumikira iwo, ndipo iwo adzasautsa izo zaka mazana anai
GENESIS 15:13 ખોજ કરો
6
GENESIS 15:2
Ndipo Abramu anati, Ambuye Mulungu, mudzandipatsa ine chiyani popeza ndine wopanda mwana, ndi amene adzakhala mwini nyumba yanga ndiye Eliyezere wa ku Damasiko?
GENESIS 15:2 ખોજ કરો
7
GENESIS 15:18
Tsiku lomwelo Yehova anapangana chipangano ndi Abramu, nati, Ndidzapatsa mbeu zako dziko ili, kuyambira pa mtsinje wa ku Ejipito kufikira pa mtsinje waukulu, mtsinje wa Yufurate
GENESIS 15:18 ખોજ કરો
8
GENESIS 15:16
Koma iwo adzabweranso kuno mbadwo wachinai: pakuti mphulupulu za Aamori sizinakwaniridwe.
GENESIS 15:16 ખોજ કરો
હોમ
બાઇબલ
યોજનાઓ
વિડિઓઝ