MACHITIDWE A ATUMWI 1:8

MACHITIDWE A ATUMWI 1:8 BLPB2014

Komatu mudzalandira mphamvu, Mzimu Woyera atadza pa inu: ndipo mudzakhala mboni zanga m'Yerusalemu, ndi m'Yudeya lonse, ndi m'Samariya, ndi kufikira malekezero ake a dziko.