YouVersion Logo
Search Icon

RUTE Mau Oyamba

Mau Oyamba
Bukuli likamba nkhani ya Rute, mkazi wachimowabu amene adakwatiwa ndi mwamuna wa ku Israele. Mwamuna wake atamwalira, iye atsatira mpongozi wake Naomi ku Betelehemu kwao chifukwa chokhulupirira Mulungu mwa Aisraele.
Nkhani yabwinoyi yochitika panthawi yankhanza ya Oweruza ija, iwonetsa kuti ngakhale amitundu nawonso adzalandira madalitso a Mulungu, akakhulupirika Mulungu wa Israele ndi kusanduka anthu ake.
Za mkatimu
Naomi abwerera ku Betelehemu pamodzi ndi Rute 1.1-22
Rute akumana ndi Bowazi 2.1—3.18
Rute akwatiwa ndi Bowazi Davide 4.1-22

Currently Selected:

RUTE Mau Oyamba: BLPB2014

Highlight

Share

Copy

None

Want to have your highlights saved across all your devices? Sign up or sign in