YouVersion Logo
Search Icon

NEHEMIYA 7:1-2

NEHEMIYA 7:1-2 BLPB2014

Ndipo atatha kumanga linga, ndinaika zitseko, nakhazika odikira, ndi oimbira, ndi Alevi; ndipo ndinawapatsa mbale wanga Hanani, ndi Hananiya kazembe wa kuboma, ulamuliro wa pa Yerusalemu; popeza ndiye munthu wokhulupirika, naposa ambiri pakuopa Mulungu.

Free Reading Plans and Devotionals related to NEHEMIYA 7:1-2