MATEYU 15:25-27
MATEYU 15:25-27 BLPB2014
Koma iye anadza, namgwadira Iye, nanena, Ambuye, ndithangateni ine. Ndipo Iye anayankha, nati, Sichabwino kutenga mkate wa ana, ndi kuuponyera tiagalu. Koma iye anati, Etu, Ambuye, pakutinso tiagalu timadya nyenyeswa zakugwa pagome pa ambuye ao.