YouVersion Logo
Search Icon

YOSWA 8:1

YOSWA 8:1 BLPB2014

Pamenepo Yehova anati kwa Yoswa, Usaope, kapena kutenga nkhawa, tenga anthu onse a nkhondo apite nawe, ndipo tauka, kwera ku Ai; taona, ndapereka m'dzanja lako mfumu ya ku Ai, ndi anthu ake ndi mudzi wake ndi dziko lake