YEREMIYA 9:13-14
YEREMIYA 9:13-14 BLPB2014
Ndipo Yehova ati, Chifukwa asiya chilamulo changa ndinachiika pamaso pao, ndipo sanamvera mau anga, osayenda m'menemo; koma anatsata kuuma kwa mtima wao, ndi Baala, monga makolo ao anawaphunzitsa