HOSEYA 2:19-20
HOSEYA 2:19-20 BLPB2014
Ndipo ndidzakutomera ukhale wanga kosatha, inde ndidzakutomera ukhale wanga m'chilungamo, ndi m'chiweruzo, ndi m'ukoma mtima, ndi m'chifundo. Ndidzakutomeranso ukhale wanga mokhulupirika, ndipo udzadziwa Yehova.