EZARA 9:9
EZARA 9:9 BLPB2014
Popeza ife ndife akapolo, koma Mulungu wathu sanatisiye m'ukapolo wathu, natifikitsira chifundo pamaso pa mafumu a Persiya, kuti atitsitsimutse kuimika nyumba ya Mulungu wathu, ndi kukonzanso muunda wake, ndi kutipatsa linga m'Yuda ndi m'Yerusalemu.