EKSODO 21:23-25
EKSODO 21:23-25 BLPB2014
Koma ngati kuphweteka kukalipo, uzipereka moyo kulipa moyo, diso kulipa diso, dzino kulipa dzino, dzanja kulipa dzanja, phazi kulipa phazi, kutentha kulipa kutentha, bala kulipa bala, mkwapulo kulipa mkwapulo.