DEUTERONOMO 30:17-18
DEUTERONOMO 30:17-18 BLPB2014
Koma mukatembenukira mtima wanu, osamvera inu, nimukacheteka, ndi kugwadira milungu ina ndi kuitumikira; ndikulalikirani inu lero, kuti mudzatayika ndithu, masiku anu sadzachuluka m'dziko limene muolokera Yordani kulowamo kulilandira.