MACHITIDWE A ATUMWI 7:57-58
MACHITIDWE A ATUMWI 7:57-58 BLPB2014
Koma anafuula ndi mau akulu, natseka m'makutu mwao, namgumukira iye ndi mtima umodzi; ndipo anamtaya kunja kwa mudzi, namponya miyala; ndipo mbonizo zinaika zovala zao pa mapazi a mnyamata dzina lake Saulo.