MACHITIDWE A ATUMWI 7:49
MACHITIDWE A ATUMWI 7:49 BLPB2014
Thambo la kumwamba ndilo mpando wachifumu wanga, ndi dziko lapansi chopondapo mapazi anga. Mudzandimangira nyumba yotani, ati Ambuye, kapena malo a mpumulo wanga ndi otani?