MACHITIDWE A ATUMWI 4:13
MACHITIDWE A ATUMWI 4:13 BLPB2014
Koma pakuona kulimbika mtima kwa Petro ndi Yohane, ndipo pozindikira kuti ndiwo anthu osaphunzira ndi opulukira, anazizwa ndipo anawazindikira, kuti adakhala pamodzi ndi Yesu.