MACHITIDWE A ATUMWI 24:25
MACHITIDWE A ATUMWI 24:25 BLPB2014
Ndipo m'mene anamfotokozera za chilungamo, ndi chidziletso, ndi chiweruziro chilinkudza, Felikisi anagwidwa ndi mantha, nayankha, Pita tsopano; ndipo ndikaona nthawi, ndidzakuitana iwe.