1 MAFUMU 3:14
1 MAFUMU 3:14 BLPB2014
Ndipo ukadzayenda m'njira zanga kusunga malemba anga ndi malamulo anga, monga atate wako Davide anayendamo, Ine ndidzachulukitsa masiku ako.