1 MAFUMU 10:1
1 MAFUMU 10:1 BLPB2014
Ndipo atamva mfumu yaikazi ya ku Sheba mbiri ya Solomoni yakubukitsa dzina la Yehova, anadza kumuyesera iye ndi miyambi yododometsa.