1
MASALIMO 79:9
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Tithandizeni Mulungu wa chipulumutso chathu, chifukwa cha ulemerero wa dzina lanu; ndipo tilanditseni, ndi kutifafanizira zoipa zathu, chifukwa cha dzina lanu.
Compare
Explore MASALIMO 79:9
2
MASALIMO 79:13
Potero ife anthu anu ndi nkhosa zapabusa panu tidzakuyamikani kosatha; tidzafotokozera chilemekezo chanu ku mibadwomibadwo.
Explore MASALIMO 79:13
3
MASALIMO 79:8
Musakumbukire motitsutsa mphulupulu za makolo athu; nsoni zokoma zanu zitipeze msanga, pakuti tafooka kwambiri.
Explore MASALIMO 79:8
Home
Bible
Plans
Videos