1
MASALIMO 76:11
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Windani ndipo chitirani Yehova Mulungu wanu zowindazo; onse akumzinga abwere nacho chopereka cha kwa Iye amene ayenera kumuopa.
Compare
Explore MASALIMO 76:11
2
MASALIMO 76:12
Iye adzadula mzimu wa akulu; akhala woopsa kwa mafumu a pa dziko lapansi.
Explore MASALIMO 76:12
Home
Bible
Plans
Videos