1
NEHEMIYA 10:39
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Pakuti ana a Israele ndi ana a Levi, azibwera nayo nsembe yokweza yatirigu, ndi yavinyo ndi yamafuta, kuzipinda kuli zipangizo za malo opatulika, ndi ansembe akutumikira, ndi odikira, ndi oimbira; kuti tisasiye nyumba ya Mulungu wathu.
Compare
Explore NEHEMIYA 10:39
2
NEHEMIYA 10:35
ndi kubwera nazo zipatso zoyamba za nthaka, ndi zoyamba za zipatso zonse za mtengo uliwonse chaka ndi chaka, ku nyumba ya Yehova
Explore NEHEMIYA 10:35
Home
Bible
Plans
Videos