1
MARKO 1:35
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo m'mawa mwake anauka usikusiku, natuluka namuka kuchipululu, napemphera kumeneko.
Compare
Explore MARKO 1:35
2
MARKO 1:15
nanena, Nthawi yakwanira, ndipo Ufumu wa Mulungu wayandikira; tembenukani mtima, khulupirirani Uthenga Wabwino.
Explore MARKO 1:15
3
MARKO 1:10-11
Ndipo pomwepo, alimkukwera potuluka m'madzi, anaona Iye thambo litang'ambika, ndi Mzimu alikutsikira pa Iye monga nkhunda: ndipo mau anatuluka m'thambo, Mwana wanga wokondedwa ndiwe, mwa Iwe ndikondwera bwino.
Explore MARKO 1:10-11
4
MARKO 1:8
Ndakubatizani inu ndi madzi; koma Iye adzakubatizani ndi Mzimu Woyera.
Explore MARKO 1:8
5
MARKO 1:17-18
Ndipo Yesu ananena nao, Idzani pambuyo panga, ndipo ndidzakusandutsani inu asodzi a anthu. Ndipo pomwepo anasiya makoka ao, namtsata Iye.
Explore MARKO 1:17-18
6
MARKO 1:22
Ndipo anazizwa ndi chiphunzitso chake; pakuti anaphunzitsa monga mwini mphamvu, si monga alembi.
Explore MARKO 1:22
Home
Bible
Plans
Videos