1
MALIRO 1:1
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Ha! Mudziwo unadzala anthu, ukhalatu pa wokha! Ukunga mkazi wamasiye! Waukuluwo mwa amitundu, kalonga wamkazi m'madera a dziko wasanduka wolamba!
Compare
Explore MALIRO 1:1
2
MALIRO 1:2
Uliralira usiku; misozi yake ili pa masaya ake; mwa onse amene anaukonda mulibe mmodzi wakuutonthoza: Mabwenzi ake onse auchitira ziwembu, asanduka adani ake.
Explore MALIRO 1:2
3
MALIRO 1:20
Onani, Yehova; pakuti ndavutika, m'kati mwanga mugwedezeka; mtima wanga wasanduka mwa ine; pakuti ndapikisana nanu ndithu; kunjako lupanga limangopha ana; m'nyumba muli imfa.
Explore MALIRO 1:20
Home
Bible
Plans
Videos