1
YOSWA 2:11
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo titamva ichi mitima yathu inasungunuka; analibenso mtima ndi mmodzi yense, chifukwa cha inu; pakuti Yehova Mulungu wanu, ndiye Mulungu wa m'mwamba umo, ndi pa dziko lapansi.
Compare
Explore YOSWA 2:11
2
YOSWA 2:10
Popeza tidamva kuti Yehova anaphwetsa madzi a m'Nyanja Yofiira pamaso panu, muja mudatuluka m'Ejipito; ndi chija munachitira mafumu awiri a Aamori okhala tsidya la Yordani, ndiwo Sihoni ndi Ogi, amene mudawaononga konse.
Explore YOSWA 2:10
3
YOSWA 2:8-9
Koma asanagone iwo, anawakwerera patsindwi iye, nati kwa amunawo, Ndidziwa kuti Yehova wakupatsani dzikoli, ndi kuti kuopsa kwanu kwatigwera, ndi kuti okhala m'dziko onse asungunuka pamaso panu.
Explore YOSWA 2:8-9
Home
Bible
Plans
Videos