1
YEREMIYA 42:6
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ngakhale ali abwino, ngakhale ali oipa, ife tidzamvera mau a Yehova Mulungu wathu, kwa Iye amene tikutumizani inu; kuti kutikomere, pomvera mau a Yehova Mulungu wathu.
Compare
Explore YEREMIYA 42:6
2
YEREMIYA 42:11-12
Musaope mfumu ya ku Babiloni, amene mumuopa; musamuope, ati Yehova: pakuti Ine ndili ndi inu kukupulumutsani, ndi kukulanditsani m'dzanja lake. Ndipo ndidzakuchitirani inu chifundo, kuti iye akuchitireni inu chifundo, nakubwezereni inu kudziko lanu.
Explore YEREMIYA 42:11-12
3
YEREMIYA 42:3
kuti Yehova Mulungu wanu atisonyeze ife njira imene tiyendemo, ndi chomwe tichite.
Explore YEREMIYA 42:3
Home
Bible
Plans
Videos