1
YEREMIYA 19:15
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele atero, Taonani, ndidzatengera mudzi uwu ndi midzi yake yonse choipa chonse chimene ndaunenera; chifukwa anaumitsa khosi lao, kuti asamve mau anga.
Compare
Explore YEREMIYA 19:15
2
YEREMIYA 19:5
namanga misanje ya Baala, kuti apsereze ana ao m'menemo nsembe zopsereza za Baala, chimene sindinawauza, sindinachinena, sichinalowa m'mtima mwanga
Explore YEREMIYA 19:5
3
YEREMIYA 19:4
Chifukwa andisiya Ine, nayesa malo ano achilendo, nafukizira m'menemo milungu ina, imene sanaidziwe, iwowa, ndi makolo ao ndi mafumu a Yuda; nadzaza malo ano ndi mwazi wa osachimwa
Explore YEREMIYA 19:4
Home
Bible
Plans
Videos