1
YAKOBO 5:16
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Chifukwa chake muvomerezane wina ndi mnzake machimo anu, ndipo mupempherere wina kwa mnzake kuti muchiritsidwe. Pemphero la munthu wolungama likhoza kwakukulu m'machitidwe ake.
Compare
Explore YAKOBO 5:16
2
YAKOBO 5:13
Kodi wina wa inu akumva zowawa? Apemphere. Kodi wina asekera? Aimbire.
Explore YAKOBO 5:13
3
YAKOBO 5:15
ndipo pemphero la chikhulupiriro lidzapulumutsa wodwalayo, ndipo Ambuye adzamuukitsa; ndipo ngati adachita machimo adzakhululukidwa kwa iye.
Explore YAKOBO 5:15
4
YAKOBO 5:14
Pali wina kodi adwala mwa inu? Adziitanire akulu a Mpingo, ndipo apemphere pa iye, atamdzoza ndi mafuta m'dzina la Ambuye
Explore YAKOBO 5:14
5
YAKOBO 5:20
azindikire, kuti iye amene abweza wochimwa kunjira yake yosochera adzapulumutsa munthu kwa imfa, ndipo adzavundikira machimo aunyinji.
Explore YAKOBO 5:20
Home
Bible
Plans
Videos