1
EZEKIELE 11:19
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo ndidzawapatsa mtima umodzi, ndi kuika mzimu watsopano m'kati mwao; ndipo ndidzawachotsera mtima wamwala m'thupi mwao, ndi kuwapatsa mtima wamnofu
Compare
Explore EZEKIELE 11:19
2
EZEKIELE 11:20
kuti ayende m'malemba anga, ndi kusunga maweruzo anga, ndi kuwachita; ndipo adzakhala anthu anga, ndi Ine ndidzakhala Mulungu wao.
Explore EZEKIELE 11:20
3
EZEKIELE 11:17
Chifukwa chake uziti, Atero Yehova Mulungu, Ndidzakumemezani kumitundu ya anthu, ndi kukusonkhanitsani muchoke m'maiko m'mene munabalalikiramo, ndipo ndidzakuninkhani dziko la Israele.
Explore EZEKIELE 11:17
Home
Bible
Plans
Videos