1
EKSODO 23:25-26
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Ndipo muzitumikira Yehova Mulungu wanu, potero adzadalitsa chakudya chako, ndi madzi ako; ndipo ndidzachotsa nthenda pakati pa iwe. M'dziko mwanu simudzakhala wakutaya mwana, kapena wosabala; ndidzakwaniritsa kuwerenga kwa masiku ako.
Compare
Explore EKSODO 23:25-26
2
EKSODO 23:20
Taona, ndituma mthenga akutsogolere, kukusunga panjira, ndi kukufikitsa pamaso pomwe ndakonzeratu.
Explore EKSODO 23:20
3
EKSODO 23:22
Pakuti ukamveratu mau ake, ndi kuchita zonse ndizilankhula, ndidzakhala mdani wa adani ako, ndipo ndidzasautsa akusautsa iwe.
Explore EKSODO 23:22
4
EKSODO 23:2-3
Usatsata unyinji wa anthu kuchita choipa; kapena usachita umboni kumlandu, ndi kupatukira kutsata unyinji ndi kukhotetsa mlandu; kapena usakometsera munthu wosauka pa mlandu wake.
Explore EKSODO 23:2-3
5
EKSODO 23:1
Usatola mbiri yopanda pake; usathandizana naye woipa ndi kukhala mboni yochititsa chiwawa.
Explore EKSODO 23:1
Home
Bible
Plans
Videos