1
DEUTERONOMO 26:19
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
kuti akukulitseni koposa amitundu onse anawalenga, wolemekezeka, womveka dzina, ndi waulemu; ndi kuti mukhale mtundu wa anthu wopatulikira Yehova Mulungu wanu monga ananena.
Compare
Explore DEUTERONOMO 26:19
2
DEUTERONOMO 26:18
Ndipo Yehova wakulonjezetsani lero kuti mudzakhala anthu akeake a pa okha, monga ananena ndi inu, ndi kuti mudzasunga malamulo ake onse
Explore DEUTERONOMO 26:18
Home
Bible
Plans
Videos