1
DANIELE 1:8
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Koma Daniele anatsimikiza mtima kuti asadzidetse ndi chakudya cha mfumu, kapena ndi vinyo amamwa; chifukwa chake anapempha mkulu wa adindo amlole asadzidetse.
Compare
Explore DANIELE 1:8
2
DANIELE 1:17
Koma anyamata amene anai, Mulungu anawapatsa chidziwitso ndi luntha la m'mabuku ali onse, ndi nzeru; koma Daniele anali nalo luntha la m'masomphenya ndi maloto onse.
Explore DANIELE 1:17
3
DANIELE 1:9
Ndipo Mulungu anamkometsera Daniele mtima wa mkulu wa adindo, amchitire chifundo.
Explore DANIELE 1:9
4
DANIELE 1:20
Ndipo m'mau ali onse anzeru ndi aluntha, amene mfumu inawafunsira. Inawapeza akuposa alembi ndi openda onse m'ufumu wake wonse.
Explore DANIELE 1:20
Home
Bible
Plans
Videos