ndi kuti,
Pita kwa anthu awa, nuti,
Ndi kumva mudzamva, ndipo simudzazindikira konse;
ndipo pakupenya mudzapenya, koma osaona konse;
pakuti mtima wa anthu awa watupatu,
ndipo m'makutu mwao mmolema kumva,
ndipo maso ao anawatseka;
kuti angaone ndi maso,
nangamve ndi makutu,
nangazindikire ndi mtima,
nangatembenuke,
ndipo Ine ndingawachiritse.