1
MACHITIDWE A ATUMWI 27:25
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Chifukwa chake, limbikani mtima, amuna inu; pakuti ndikhulupirira Mulungu, kuti kudzatero monga momwe ananena ndi ine.
Compare
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 27:25
2
MACHITIDWE A ATUMWI 27:23-24
Pakuti anaimirira kwa ine usiku walero mngelo wa Mulungu amene ndili wake, amenenso ndimtumikira, nanena, Usaope Paulo; ukaimirira pamaso pa Kaisara; ndipo, taona, Mulungu anakupatsa onse amene akuyenda nawe pamodzi.
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 27:23-24
3
MACHITIDWE A ATUMWI 27:22
Koma tsopano ndikuchenjezani mulimbike mtima; pakuti sadzatayika wamoyo mmodzi mwa inu, koma ngalawa ndiyo.
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 27:22
Home
Bible
Plans
Videos