1
MACHITIDWE A ATUMWI 22:16
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo tsopano uchedweranji? Tauka, nubatizidwe ndi kusamba kuchotsa machimo ako, nuitane pa dzina lake.
Compare
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 22:16
2
MACHITIDWE A ATUMWI 22:14
Ndipo anati, Mulungu wa makolo athu anakusankhiratu udziwe chifuniro chake, nuone Wolungamayo, numve mau otuluka m'kamwa mwake.
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 22:14
3
MACHITIDWE A ATUMWI 22:15
Ndipo udzamkhalira Iye mboni kwa anthu onse, za izo udaziona ndi kuzimva.
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 22:15
Home
Bible
Plans
Videos