1
2 MAFUMU 3:17
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Pakuti atero Yehova, Simudzaona mphepo, kapena kuona mvula, koma chigwacho chidzadzala ndi madzi; ndipo mudzamwa inu, ndi ng'ombe zanu, ndi zoweta zanu.
Compare
Explore 2 MAFUMU 3:17
2
2 MAFUMU 3:15
Koma tsopano, nditengereni wanthetemya. Ndipo kunali, wanthetemyayo ali chiimbire, dzanja la Yehova linamgwera.
Explore 2 MAFUMU 3:15
Home
Bible
Plans
Videos