1
1 MAFUMU 4:29
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo Mulungu anampatsa Solomoni nzeru ndi luntha lambiri, ndi mtima wodziwa za mitundumitundu, zonga mchenga uli m'mphepete mwa nyanja.
Compare
Explore 1 MAFUMU 4:29
2
1 MAFUMU 4:34
Ndipo anafikapo anthu a mitundu yonse kudzamva nzeru ya Solomoni, ochokera kwa mafumu onse a dziko lonse lapansi, amene adamva mbiri ya nzeru yake.
Explore 1 MAFUMU 4:34
Home
Bible
Plans
Videos