1 MAFUMU 4:29
1 MAFUMU 4:29 BLPB2014
Ndipo Mulungu anampatsa Solomoni nzeru ndi luntha lambiri, ndi mtima wodziwa za mitundumitundu, zonga mchenga uli m'mphepete mwa nyanja.