1
1 MAFUMU 14:8
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
ndipo ndinalanda nyumba ya Davide ufumu, ndi kuupereka kwa iwe, koma sunafanana ndi Davide mtumiki wanga uja, amene anasunga malamulo anga, nanditsata ndi mtima wake wonse kuchita zolunjika zokhazokha pamaso panga
Compare
Explore 1 MAFUMU 14:8
2
1 MAFUMU 14:9
koma wachimwa koposa onse akale, nukadzipangira milungu ina ndi mafano yoyenga kundikwiyitsa, nunditaya Ine kumbuyo kwako
Explore 1 MAFUMU 14:9
Home
Bible
Plans
Videos