1
1 MAFUMU 11:4
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo kunali, atakalamba Solomoni, akazi ake anapambutsa mtima wake atsate milungu ina; ndipo mtima wake sunakhala wangwiro ndi Yehova Mulungu wake monga mtima wa Davide atate wake.
Compare
Explore 1 MAFUMU 11:4
2
1 MAFUMU 11:9
Ndipo Yehova anakwiya ndi Solomoni, pokhala mtima wake unapatuka kwa Yehova Mulungu wa Israele, amene adamuonekera kawiri
Explore 1 MAFUMU 11:9
Home
Bible
Plans
Videos