1
Machitidwe a Atumwi 7:59-60
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Akumugenda miyala, Stefano anapemphera kuti, “Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga.” Ndipo anagwada pansi nafuwula mwamphamvu kuti, “Ambuye musawawerengere tchimoli.” Atanena mawu amenewa anamwalira.
Compare
Explore Machitidwe a Atumwi 7:59-60
2
Machitidwe a Atumwi 7:49
“ ‘Kumwamba ndi mpando wanga waufumu, ndipo dziko lapansi ndi chopondapo mapazi anga. Kodi mudzandimangira nyumba yotani? Akutero Ambuye. Kapena malo opumuliramo Ine ali kuti?
Explore Machitidwe a Atumwi 7:49
3
Machitidwe a Atumwi 7:57-58
Koma iwo anatseka mʼmakutu mwawo, ndipo anafuwula kolimba, onse anathamangira kwa iye, anamukokera kunja kwa mzinda ndipo anayamba kumugenda miyala. Mboni zinasungitsa zovala zawo kwa mnyamata otchedwa Saulo.
Explore Machitidwe a Atumwi 7:57-58
Home
Bible
Plans
Videos