1
Machitidwe a Atumwi 6:3-4
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Choncho abale, sankhani pakati panu anthu asanu ndi awiri a mbiri yabwino, odzazidwa ndi Mzimu Woyera ndi anzeru. Ife tidzawapatsa udindo oyangʼanira. Koma ife tidzadzipereka kuti tizipemphera ndi kulalikira mawu.”
Compare
Explore Machitidwe a Atumwi 6:3-4
2
Machitidwe a Atumwi 6:7
Ndipo Mawu a Mulungu anapitirira kufalikira. Chiwerengero cha ophunzira mu Yerusalemu chinakula mofulumira ndipo ansembe ochuluka anakhulupirira.
Explore Machitidwe a Atumwi 6:7
Home
Bible
Plans
Videos