1
MACHITIDWE 10:34-35
Buku Lopatulika
Ndipo Petro anatsegula pakamwa pake, nati, Zoona ndizindikira kuti Mulungu alibe tsankho; koma m'mitundu yonse, wakumuopa Iye ndi wakuchita chilungamo alandiridwa naye.
Compare
Explore MACHITIDWE 10:34-35
2
MACHITIDWE 10:43
Ameneyu aneneri onse amchitira umboni, kuti onse akumkhulupirira Iye adzalandira chikhululukiro cha machimo ao, mwa dzina lake.
Explore MACHITIDWE 10:43
Home
Bible
Plans
Videos