YouVersion Logo
Search Icon

MACHITIDWE 10:34-35

MACHITIDWE 10:34-35 BLP-2018

Ndipo Petro anatsegula pakamwa pake, nati, Zoona ndizindikira kuti Mulungu alibe tsankho; koma m'mitundu yonse, wakumuopa Iye ndi wakuchita chilungamo alandiridwa naye.