1
GENESIS 5:24
Buku Lopatulika
ndipo Enoki anayendabe ndi Mulungu; ndipo panalibe iye; pakuti Mulungu anamtenga.
對照
GENESIS 5:24 探索
2
GENESIS 5:22
ndipo Enoki anayendabe ndi Mulungu, atabala Metusela, zaka mazana atatu, nabala ana aamuna ndi aakazi
GENESIS 5:22 探索
3
GENESIS 5:1
Ili ndi buku la mibadwo ya Adamu. Tsiku lomwe Mulungu analenga munthu anamlenga m'chifanizo cha Mulungu
GENESIS 5:1 探索
4
GENESIS 5:2
anawalenga iwo mwamuna ndi mkazi, nawadalitsa iwo natcha mtundu wao anthu, tsiku lomwe anawalenga iwo.
GENESIS 5:2 探索
主頁
聖經
計劃
影片