YouVersion Logo
تلاش

YOHANE 11:43-44

YOHANE 11:43-44 BLPB2014

Ndipo m'mene adanena izi, anafuula ndi mau akulu, Lazaro, tuluka. Ndipo womwalirayo anatuluka womangidwa miyendo ndi manja ndi nsalu za kumanda; ndi nkhope yake inazingidwa ndi mlezo. Yesu ananena nao, Mmasuleni iye, ndipo mlekeni amuke.

پڑھیں YOHANE 11

سنیں YOHANE 11