Gen. 37:6-7
Gen. 37:6-7 BLY-DC
Iye adaŵauza kuti “Mverani maloto omwe ndalota. Tonsefe tinali m'munda, ndipo tinalikumanga mitolo yatirigu. Tilikumanga chomwecho, mtolo wanga unaimirira. Tsono mitolo yanu inauzungulira mtolo wangawo ndi kumauŵeramira.”