Gen. 35:11-12

Gen. 35:11-12 BLY-DC

Pambuyo pake Mulungu adamuuza kuti, “Ine ndine Mulungu, Mphambe. Ubale ana ambiri. Udzakhala ndi zidzukulu zambiri, ndipo zina mwa izo zidzakhala mafumu. Zidzukulu zako zidzachuluka kwambiri, kotero kuti zidzakhala mitundu yambiri ya anthu. Ndidzakupatsa dziko limene ndidapatsa Abrahamu ndi Isaki. Dziko limeneli ndidzapatsanso zidzukulu zako, iwe utafa.”

อ่าน Gen. 35

วิดีโอสำหรับ Gen. 35:11-12