Gen. 25:32-33
Gen. 25:32-33 BLY-DC
Esau adati, “Chabwino, inetu ndili pafupi kufa. Kodi ukulu wangawo udzandipinduliranji?” Yakobe adati, “Uyambe walumbira kuti ukulu wakowo wandipatsadi.” Apo Esau adalumbira, nagulitsa ukulu wake wauchisamba kwa Yakobe.